Genesis 36:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ana a Zibeoni anali Aya ndi Ana. Uyu ndi Ana amene anapeza akasupe a madzi otentha m’chipululu, pamene anali kudyetsa abulu a Zibeoni bambo ake.+
24 Ana a Zibeoni anali Aya ndi Ana. Uyu ndi Ana amene anapeza akasupe a madzi otentha m’chipululu, pamene anali kudyetsa abulu a Zibeoni bambo ake.+