Genesis 36:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Esau anatenga akazi pakati pa ana aakazi a ku Kanani.+ Anatenga Ada,+ mwana wamkazi wa Eloni, Mhiti.+ Anatenganso Oholibama,+ yemwe anali mwana wamkazi wa Ana, komanso anali mdzukulu wa Zibeoni, Mhivi.
2 Esau anatenga akazi pakati pa ana aakazi a ku Kanani.+ Anatenga Ada,+ mwana wamkazi wa Eloni, Mhiti.+ Anatenganso Oholibama,+ yemwe anali mwana wamkazi wa Ana, komanso anali mdzukulu wa Zibeoni, Mhivi.