Genesis 36:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Nawa tsopano mafumu aakulu amene analamulira dziko la Edomu,+ ana a Isiraeli asanayambe kulamulidwa ndi mfumu ina iliyonse:+
31 Nawa tsopano mafumu aakulu amene analamulira dziko la Edomu,+ ana a Isiraeli asanayambe kulamulidwa ndi mfumu ina iliyonse:+