Deuteronomo 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Ukakafika m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, n’kulitengadi kukhala lako ndi kukhalamo,+ pamenepo iwe n’kunena kuti, ‘Ndidziikire mfumu ngati mitundu ina yonse yondizungulira,’+ Deuteronomo 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 uzidziikira mfumu imene Yehova Mulungu wako adzasankhe.+ Mfumu imene udzadziikire idzachokere pakati pa abale ako. Sudzaloledwa kudziikira mlendo amene si m’bale wako kukhala mfumu. 1 Samueli 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma inu, lero mwakana Mulungu wanu+ amene anakupulumutsani m’masautso anu onse ndi m’zowawa zanu, kufika ponena kuti: “Ife tikufuna kuti utiikire mfumu yoti izitilamulira.” Tsopano imani pamaso pa Yehova malinga ndi mafuko anu+ ndi mabanja anu.’”*
14 “Ukakafika m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, n’kulitengadi kukhala lako ndi kukhalamo,+ pamenepo iwe n’kunena kuti, ‘Ndidziikire mfumu ngati mitundu ina yonse yondizungulira,’+
15 uzidziikira mfumu imene Yehova Mulungu wako adzasankhe.+ Mfumu imene udzadziikire idzachokere pakati pa abale ako. Sudzaloledwa kudziikira mlendo amene si m’bale wako kukhala mfumu.
19 Koma inu, lero mwakana Mulungu wanu+ amene anakupulumutsani m’masautso anu onse ndi m’zowawa zanu, kufika ponena kuti: “Ife tikufuna kuti utiikire mfumu yoti izitilamulira.” Tsopano imani pamaso pa Yehova malinga ndi mafuko anu+ ndi mabanja anu.’”*