Genesis 36:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Bela mwana wa Beori analamulira Edomu,+ ndipo dzina la mzinda wake linali Dinihaba.