Genesis 36:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Shauli atamwalira, Baala-hanani mwana wa Akibori, anayamba kulamulira m’malo mwake.+