Genesis 41:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Patapita zaka ziwiri zathunthu, Farao analota maloto.+ Analota kuti waimirira m’mbali mwa mtsinje wa Nailo. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:1 Nsanja ya Olonda,2/1/2015, tsa. 14
41 Patapita zaka ziwiri zathunthu, Farao analota maloto.+ Analota kuti waimirira m’mbali mwa mtsinje wa Nailo.