Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 20:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pambuyo pake Mulungu anafikira Abimeleki usiku m’maloto n’kumuuza kuti: “Ufatu iwe chifukwa cha mkazi amene watengayu,+ pakuti ndi mkazi wa mwini.”+

  • Genesis 40:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Usiku wina,+ woperekera chikho ndi wophika mkate, atumiki a mfumu ya Iguputo omwe anali m’ndende+ aja, analota maloto.+ Aliyense analota maloto ake okhala ndi tanthauzo lakelake.+

  • Yobu 33:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Iye amawalankhula m’maloto+ ndi m’masomphenya+ a usiku,

      Anthu akakhala m’tulo tofa nato,

      Akamagona pabedi.+

  • Danieli 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 M’chaka chachiwiri cha ufumu wa Nebukadinezara, Nebukadinezarayo analota maloto.+ Malotowo anamuvutitsa maganizo+ ndipo tulo tinamuthera.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena