Genesis 42:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pamenepo Yakobo bambo wawo anadandaula kuti: “Inetu mwandisandutsa namfedwa!+ Yosefe anapita, Simiyoni kulibenso.+ Tsopano mukufuna kutenga Benjamini! Masoka onsewa akugwera ine!”
36 Pamenepo Yakobo bambo wawo anadandaula kuti: “Inetu mwandisandutsa namfedwa!+ Yosefe anapita, Simiyoni kulibenso.+ Tsopano mukufuna kutenga Benjamini! Masoka onsewa akugwera ine!”