Genesis 45:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atatero, anayamba kulira mokweza mawu+ mpaka Aiguputo anamva, ndiponso a kunyumba ya Farao anamva zakuti Yosefe akulira.
2 Atatero, anayamba kulira mokweza mawu+ mpaka Aiguputo anamva, ndiponso a kunyumba ya Farao anamva zakuti Yosefe akulira.