Genesis 45:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mukatenge bambo anu ndi mabanja anu n’kubwera nawo kuno kwa ine. Ndidzakupatsani zabwino za dziko la Iguputo, ndipo mudzadya zonona za dzikoli.+
18 Mukatenge bambo anu ndi mabanja anu n’kubwera nawo kuno kwa ine. Ndidzakupatsani zabwino za dziko la Iguputo, ndipo mudzadya zonona za dzikoli.+