Genesis 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Rabekayo anayankha kuti: “Eni, imwani mbuyanga.” Atatero anatsitsa mtsuko wake mwamsanga n’kuupendeketsa kuti mtumikiyo amwe.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:18 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2016, tsa. 12
18 Rabekayo anayankha kuti: “Eni, imwani mbuyanga.” Atatero anatsitsa mtsuko wake mwamsanga n’kuupendeketsa kuti mtumikiyo amwe.+