Genesis 26:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 M’mawa mwake, analawirira kudzuka n’kulumbiritsana.+ Kenako Isaki anatsanzikana nawo ndipo iwo anachoka kwa iye mwamtendere.+
31 M’mawa mwake, analawirira kudzuka n’kulumbiritsana.+ Kenako Isaki anatsanzikana nawo ndipo iwo anachoka kwa iye mwamtendere.+