Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 14:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Koma Abulamu anauza mfumu ya ku Sodomuyo kuti: “Ndikukweza manja anga kulumbira+ kwa Yehova Mulungu Wam’mwambamwamba, Amene anapanga kumwamba ndi dziko lapansi.

  • Genesis 21:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Chotero lumbira panopo kuti, pali Mulungu+ udzakhala wokhulupirika kwa ine, kwa ana anga ndi kwa mbadwa zanga.+ Ndiponso kuti udzatero chifukwa cha chikondi chosatha+ chimene ine ndakusonyeza. Choncho udzandichitira ine motero, pamodzi ndi dziko limene ukukhalamo monga mlendoli.”+

  • 1 Samueli 20:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho Yonatani analumbiranso kwa Davide chifukwa chakuti anali kum’konda kwambiri. Pakuti Yonatani anali kukonda Davide monga mmene anali kudzikondera iye mwini.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena