1 Samueli 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Davide atangomaliza kulankhula ndi Sauli, Yonatani+ anagwirizana kwambiri+ ndi Davide, moti anayamba kukonda Davide ngati mmene anali kudzikondera yekha.+ 2 Samueli 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mtima wanga ukuwawa chifukwa cha iwe m’bale wanga Yonatani,Unali wosangalatsa kwambiri kwa ine.+Chikondi chako chinali chapamwamba kwambiri kuposa chikondi cha akazi.+ Miyambo 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pali mabwenzi amene amafuna kuthyolana,+ koma pali bwenzi limene limamatirira kuposa m’bale wako.+
18 Ndiyeno Davide atangomaliza kulankhula ndi Sauli, Yonatani+ anagwirizana kwambiri+ ndi Davide, moti anayamba kukonda Davide ngati mmene anali kudzikondera yekha.+
26 Mtima wanga ukuwawa chifukwa cha iwe m’bale wanga Yonatani,Unali wosangalatsa kwambiri kwa ine.+Chikondi chako chinali chapamwamba kwambiri kuposa chikondi cha akazi.+
24 Pali mabwenzi amene amafuna kuthyolana,+ koma pali bwenzi limene limamatirira kuposa m’bale wako.+