Genesis 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Esau anafunsa kuti: “Nanga n’chifukwa chiyani watumiza khamu lonse limene ndakumana nalo lija?”+ Poyankha iye anati: “Ndachita zimenezi kuti mundikomere mtima mbuyanga.”+
8 Tsopano Esau anafunsa kuti: “Nanga n’chifukwa chiyani watumiza khamu lonse limene ndakumana nalo lija?”+ Poyankha iye anati: “Ndachita zimenezi kuti mundikomere mtima mbuyanga.”+