Genesis 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’kupita kwa nthawi Ada anabereka Yabala, amene anakhala tate wa anthu okhala m’mahema+ ndi oweta ziweto.+
20 M’kupita kwa nthawi Ada anabereka Yabala, amene anakhala tate wa anthu okhala m’mahema+ ndi oweta ziweto.+