Ekisodo 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo iye anauza ana akewo kuti: “Nanga iyeyo ali kuti? Mwamusiyiranji? Pitani mukamuitane kuti adzadye chakudya.”+
20 Pamenepo iye anauza ana akewo kuti: “Nanga iyeyo ali kuti? Mwamusiyiranji? Pitani mukamuitane kuti adzadye chakudya.”+