Genesis 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Loti anawaumiriza kwambiri+ moti mpaka iwo anapita naye kunyumba kwake. Kumeneko anawakonzera phwando,+ n’kuwaphikira mikate yopanda chofufumitsa,+ ndipo anadya. Genesis 24:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Atangomuona anamuuza kuti: “Tabwerani, inu wodalitsika wa Yehova.+ Bwanji mwangoima kunja kuno? Inetu ndakonza kale malo kunyumbaku, a inu ndi a ngamilazi.” Yobu 31:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Palibe mlendo amene ankagona panja usiku.+Zitseko zanga ndinkazisiya zotsegula kwa odutsa m’njira. Aroma 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Gawanani ndi oyera malinga ndi zosowa zawo.+ Khalani ochereza.+ Aheberi 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Musaiwale kuchereza alendo,+ pakuti potero, ena anachereza angelo mosadziwa.+
3 Koma Loti anawaumiriza kwambiri+ moti mpaka iwo anapita naye kunyumba kwake. Kumeneko anawakonzera phwando,+ n’kuwaphikira mikate yopanda chofufumitsa,+ ndipo anadya.
31 Atangomuona anamuuza kuti: “Tabwerani, inu wodalitsika wa Yehova.+ Bwanji mwangoima kunja kuno? Inetu ndakonza kale malo kunyumbaku, a inu ndi a ngamilazi.”
32 Palibe mlendo amene ankagona panja usiku.+Zitseko zanga ndinkazisiya zotsegula kwa odutsa m’njira.