Ekisodo 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Muzisamalira zonse zimene ndakuuzani,+ ndipo musatchule dzina la milungu ina. Lisamveke pakamwa panu.+
13 “Muzisamalira zonse zimene ndakuuzani,+ ndipo musatchule dzina la milungu ina. Lisamveke pakamwa panu.+