Ekisodo 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Popereka magazi a nsembe yanga musawapereke limodzi ndi chilichonse chokhala ndi chofufumitsa. Ndipo mafuta a chikondwerero changa asamagone mpaka m’mawa.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:18 Nsanja ya Olonda,2/15/1990, tsa. 12
18 “Popereka magazi a nsembe yanga musawapereke limodzi ndi chilichonse chokhala ndi chofufumitsa. Ndipo mafuta a chikondwerero changa asamagone mpaka m’mawa.+