Ekisodo 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako ulikute ndi golide woyenga bwino.+ Mkati ndi kunja komwe ulikute ndi golide, ndipo upange mkombero wagolide kuzungulira Likasalo.+
11 Kenako ulikute ndi golide woyenga bwino.+ Mkati ndi kunja komwe ulikute ndi golide, ndipo upange mkombero wagolide kuzungulira Likasalo.+