Ekisodo 25:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Ndiyeno upange mbale zake, zikho, mitsuko ndi mbale zolowa zoti azithirira nsembe zachakumwa. Uzipange ndi golide woyenga bwino.+
29 “Ndiyeno upange mbale zake, zikho, mitsuko ndi mbale zolowa zoti azithirira nsembe zachakumwa. Uzipange ndi golide woyenga bwino.+