Ekisodo 25:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mupangenso mbale zake, makapu, mitsuko ndi mbale zolowa zoti azithirira nsembe zachakumwa. Muzipange ndi golide woyenga bwino.+
29 Mupangenso mbale zake, makapu, mitsuko ndi mbale zolowa zoti azithirira nsembe zachakumwa. Muzipange ndi golide woyenga bwino.+