Ekisodo 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mitengo yonyamulirayo uziilowetsa mumphetezo kumbali ziwiri za guwalo polinyamula.+