Ekisodo 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndodo zonyamulirazo uzizilowetsa mumphetezo mʼmbali zonse ziwiri za guwalo polinyamula.+