Ekisodo 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Tsopano uchite izi kwa iwo kuti uwayeretse atumikire monga ansembe anga: Utenge ng’ombe yaing’ono yamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo,+ zopanda chilema,+
29 “Tsopano uchite izi kwa iwo kuti uwayeretse atumikire monga ansembe anga: Utenge ng’ombe yaing’ono yamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo,+ zopanda chilema,+