-
2 Mbiri 13:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kodi simunathamangitse ansembe a Yehova,+ omwe ndi ana a Aroni, komanso Alevi? Ndipo kodi simukudziikira ansembe ngati mmene amachitira anthu a mayiko ena?+ Aliyense amene wabwera n’kudziika pa udindo waunsembe mwa kupereka ng’ombe yaing’ono yamphongo ndi nkhosa zamphongo 7, amakhala wansembe wa mafano omwe si milungu.+
-