Ekisodo 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Zovala zoti apange ndi izi: chovala pachifuwa,+ efodi,*+ malaya akunja odula manja,+ mkanjo wamandalasi, nduwira+ ndi lamba wa pamimba.+ Apange zovala zopatulika za Aroni m’bale wako ndi ana ake, kuti atumikire monga wansembe wanga. Ekisodo 39:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 zovala+ zosokedwa bwino zoti azivala potumikira m’malo opatulika, zovala zopatulika+ za Aroni wansembe ndi zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe.+
4 “Zovala zoti apange ndi izi: chovala pachifuwa,+ efodi,*+ malaya akunja odula manja,+ mkanjo wamandalasi, nduwira+ ndi lamba wa pamimba.+ Apange zovala zopatulika za Aroni m’bale wako ndi ana ake, kuti atumikire monga wansembe wanga.
41 zovala+ zosokedwa bwino zoti azivala potumikira m’malo opatulika, zovala zopatulika+ za Aroni wansembe ndi zovala za ana ake zoti azivala potumikira monga ansembe.+