Ekisodo 39:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno anapanga nduwira+ ya nsalu yabwino kwambiri, mipango yokongola yokulunga kumutu+ ya nsalu zabwino kwambiri ndi makabudula a nsalu+ za ulusi wopota wabwino kwambiri. Ekisodo 39:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atatero anapanga kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide woyenga bwino, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka. Analembapo mawu akuti: “Chiyero n’cha Yehova.”+ Mawuwa anawalemba mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo. Levitiko 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anamuvekanso nduwira+ pamutu pake, n’kuika patsogolo pa nduwirayo kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.
28 Ndiyeno anapanga nduwira+ ya nsalu yabwino kwambiri, mipango yokongola yokulunga kumutu+ ya nsalu zabwino kwambiri ndi makabudula a nsalu+ za ulusi wopota wabwino kwambiri.
30 Atatero anapanga kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide woyenga bwino, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka. Analembapo mawu akuti: “Chiyero n’cha Yehova.”+ Mawuwa anawalemba mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo.
9 Anamuvekanso nduwira+ pamutu pake, n’kuika patsogolo pa nduwirayo kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide, chizindikiro chopatulika cha kudzipereka,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.