Ekisodo 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Zovala zoti apange ndi izi: chovala pachifuwa,+ efodi,*+ malaya akunja odula manja,+ mkanjo wamandalasi, nduwira+ ndi lamba wa pamimba.+ Apange zovala zopatulika za Aroni m’bale wako ndi ana ake, kuti atumikire monga wansembe wanga. Ekisodo 28:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Kenako uwombe mkanjo wamandalasi ndi ulusi wabwino kwambiri. Upangenso nduwira ya nsalu yabwino kwambiri,+ ndiponso uwombe lamba+ wa mkanjo.
4 “Zovala zoti apange ndi izi: chovala pachifuwa,+ efodi,*+ malaya akunja odula manja,+ mkanjo wamandalasi, nduwira+ ndi lamba wa pamimba.+ Apange zovala zopatulika za Aroni m’bale wako ndi ana ake, kuti atumikire monga wansembe wanga.
39 “Kenako uwombe mkanjo wamandalasi ndi ulusi wabwino kwambiri. Upangenso nduwira ya nsalu yabwino kwambiri,+ ndiponso uwombe lamba+ wa mkanjo.