Ekisodo 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Zovala zoti apange ndi izi: chovala pachifuwa,+ efodi,*+ malaya akunja odula manja,+ mkanjo wamandalasi, nduwira+ ndi lamba wa pamimba.+ Apange zovala zopatulika za Aroni m’bale wako ndi ana ake, kuti atumikire monga wansembe wanga. Chivumbulutso 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye waloledwa kuvala zovala zapamwamba, zonyezimira ndi zoyera bwino, pakuti zovala zapamwambazo zikuimira ntchito zolungama za oyera.”+
4 “Zovala zoti apange ndi izi: chovala pachifuwa,+ efodi,*+ malaya akunja odula manja,+ mkanjo wamandalasi, nduwira+ ndi lamba wa pamimba.+ Apange zovala zopatulika za Aroni m’bale wako ndi ana ake, kuti atumikire monga wansembe wanga.
8 Iye waloledwa kuvala zovala zapamwamba, zonyezimira ndi zoyera bwino, pakuti zovala zapamwambazo zikuimira ntchito zolungama za oyera.”+