Ekisodo 28:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndipo uwapangire makabudula ansalu ofika m’ntchafu kuti azibisa maliseche awo.+ Ezekieli 44:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo azivala zovala za kumutu zansalu+ ndi makabudula ansalu.+ Asamavale zovala zochititsa thukuta.
18 Iwo azivala zovala za kumutu zansalu+ ndi makabudula ansalu.+ Asamavale zovala zochititsa thukuta.