Ekisodo 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ukatero utengeko magazi a ng’ombeyo+ ndi chala chako ndi kuwapaka panyanga za guwa lansembe.+ Otsalawo uwathire pansi, paguwa lansembe.+
12 Ukatero utengeko magazi a ng’ombeyo+ ndi chala chako ndi kuwapaka panyanga za guwa lansembe.+ Otsalawo uwathire pansi, paguwa lansembe.+