Ekisodo 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Upange nyanga m’makona ake anayi. Nyanga+ zakezo zituluke m’makona akewo, ndipo ulikute ndi mkuwa.+
2 Upange nyanga m’makona ake anayi. Nyanga+ zakezo zituluke m’makona akewo, ndipo ulikute ndi mkuwa.+