Levitiko 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno wansembe azitenga ena mwa magazi a nsembe yamachimoyo ndi chala chake n’kuwapaka panyanga+ za guwa lansembe zopsereza. Magazi ena onse a mbuziyo aziwathira pansi pa guwa lansembe zopsereza. 1 Mafumu 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Nkhaniyo inam’fika Yowabu,+ ndipo iye anathawira kuchihema+ cha Yehova n’kukagwira nyanga za guwa lansembe.+ Paja Yowabu ankatsatira Adoniya,+ ngakhale kuti sanatsatire+ Abisalomu. Salimo 118:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova ndiye Mulungu,+Ndipo amatipatsa kuwala.+Kongoletsani gulu la anthu amene ali pachikondwerero+ ndi nthambi za mitengo,+ anthu inu.Likongoletseni mpaka kukafika panyanga za guwa lansembe.+
25 Ndiyeno wansembe azitenga ena mwa magazi a nsembe yamachimoyo ndi chala chake n’kuwapaka panyanga+ za guwa lansembe zopsereza. Magazi ena onse a mbuziyo aziwathira pansi pa guwa lansembe zopsereza.
28 Nkhaniyo inam’fika Yowabu,+ ndipo iye anathawira kuchihema+ cha Yehova n’kukagwira nyanga za guwa lansembe.+ Paja Yowabu ankatsatira Adoniya,+ ngakhale kuti sanatsatire+ Abisalomu.
27 Yehova ndiye Mulungu,+Ndipo amatipatsa kuwala.+Kongoletsani gulu la anthu amene ali pachikondwerero+ ndi nthambi za mitengo,+ anthu inu.Likongoletseni mpaka kukafika panyanga za guwa lansembe.+