Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 38:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anapanganso nyanga+ m’makona ake anayi. Nyanga zakezo zinatuluka m’makona akewo, ndipo guwalo analikuta ndi mkuwa.+

  • Numeri 16:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 zofukizira za amuna amene anafa+ chifukwa cha kuchimwa. Azisule kuti zikhale timalata topyapyala n’kukutira nato guwa lansembe,+ popeza anafika nazo pamaso pa Yehova, ndipo zakhala zopatulika. Timalatato tikhale chikumbutso kwa ana a Isiraeli.’”+

  • 1 Mafumu 8:64
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 64 Tsiku limenelo, pakati pa bwalo la nyumba ya Yehova+ panayenera kupatulidwa ndi mfumu, chifukwa inafunika kuperekerapo nsembe yopsereza, nsembe yambewu, ndi mafuta a nsembe zachiyanjano. Inatero popeza guwa lansembe lamkuwa+ limene lili pamaso pa Yehova linachepa, ndipo nsembe yopsereza, nsembe yambewu, ndi mafuta+ a nsembe zachiyanjano sizikanakwanapo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena