-
Ekisodo 29:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Akatero, uphe nkhosayo ndi kutengako magazi ake ndi kuwapaka m’munsi pakhutu la kudzanja lamanja la Aroni, ndi m’munsi pamakutu a kudzanja lamanja a ana a Aroni. Uwapakenso pazala zawo za manthu kudzanja lamanja ndi pazala zawo zazikulu za kumwendo wa kumanja,+ ndipo uwaze magaziwo mozungulira paguwa lansembe.
-