Ekisodo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiyeno uzitenge m’manja mwawo ndi kuzitentha paguwa lansembe pamwamba pa nsembe yopsereza, kuti zikhale fungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.+ Ndiyo nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.+
25 Ndiyeno uzitenge m’manja mwawo ndi kuzitentha paguwa lansembe pamwamba pa nsembe yopsereza, kuti zikhale fungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova.+ Ndiyo nsembe yotentha ndi moto yoperekedwa kwa Yehova.+