Ekisodo 29:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 M’mibadwo yanu yonse, muzipereka nsembe yopsereza imeneyi nthawi zonse+ pakhomo la chihema chokumanako pamaso pa Yehova, kumene ndidzaonekera kwa inu kuti ndilankhule nanu.+
42 M’mibadwo yanu yonse, muzipereka nsembe yopsereza imeneyi nthawi zonse+ pakhomo la chihema chokumanako pamaso pa Yehova, kumene ndidzaonekera kwa inu kuti ndilankhule nanu.+