Ekisodo 29:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ndidzayeretsa chihema chokumanako ndi guwa lansembe. Ndidzayeretsanso+ Aroni ndi ana ake kuti atumikire monga ansembe anga.
44 Ndidzayeretsa chihema chokumanako ndi guwa lansembe. Ndidzayeretsanso+ Aroni ndi ana ake kuti atumikire monga ansembe anga.