Ekisodo 37:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anapanganso akerubi awiri agolide. Anali osula ndipo anawapanga kumapeto onse awiri a chivundikirocho.+
7 Anapanganso akerubi awiri agolide. Anali osula ndipo anawapanga kumapeto onse awiri a chivundikirocho.+