Ekisodo 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Upangenso akerubi awiri agolide. Akhale osula ndipo uwaike kumapeto onse awiri a chivundikirocho.+ Ekisodo 40:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako anatenga Umboni+ ndi kuuika mu Likasa,+ ndipo analowetsa mitengo yonyamulira+ m’mbali mwa Likasalo ndi kuika chivundikiro+ pamwamba pa Likasa.+
18 Upangenso akerubi awiri agolide. Akhale osula ndipo uwaike kumapeto onse awiri a chivundikirocho.+
20 Kenako anatenga Umboni+ ndi kuuika mu Likasa,+ ndipo analowetsa mitengo yonyamulira+ m’mbali mwa Likasalo ndi kuika chivundikiro+ pamwamba pa Likasa.+