Ekisodo 16:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Monga momwe Yehova analamulira Mose, Aroni anaikadi mtsukowo patsogolo pa Umboni*+ kuti manawo asungidwe. Ekisodo 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwapo mawu ndi chala cha Mulungu.+
34 Monga momwe Yehova analamulira Mose, Aroni anaikadi mtsukowo patsogolo pa Umboni*+ kuti manawo asungidwe.
18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwapo mawu ndi chala cha Mulungu.+