Ekisodo 40:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Udzaike guwa lansembe+ zopsereza patsogolo pa khomo la chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako.
6 “Udzaike guwa lansembe+ zopsereza patsogolo pa khomo la chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako.