Ekisodo 40:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo analowetsa Likasa m’chihema chopatulika ndi kuika nsalu yotchinga+ pamalo ake, kutchinga likasa la umboni,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.
21 Pamenepo analowetsa Likasa m’chihema chopatulika ndi kuika nsalu yotchinga+ pamalo ake, kutchinga likasa la umboni,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.