Ekisodo 40:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 kuti azifukizirapo zofukiza zonunkhira,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.