Levitiko 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atatero anabweretsa ng’ombe yamphongo+ ya nsembe yamachimo, ndipo Aroni ndi ana ake anaika manja awo pamutu+ pa ng’ombe ya nsembe yamachimoyo.
14 Atatero anabweretsa ng’ombe yamphongo+ ya nsembe yamachimo, ndipo Aroni ndi ana ake anaika manja awo pamutu+ pa ng’ombe ya nsembe yamachimoyo.