Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Kenako upereke ng’ombe patsogolo pa chihema chokumanako, ndipo Aroni ndi ana ake aike manja awo pamutu wa ng’ombeyo.+

  • Levitiko 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “‘Ngati wansembe, wodzozedwa,+ wachita tchimo+ limene lapalamulitsa anthu onse, azipereka kwa Yehova ng’ombe yaing’ono yamphongo yopanda chilema monga nsembe yamachimo chifukwa cha tchimo lakelo.+

  • Levitiko 16:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Ndiponso Aroni azitenga ng’ombe yamphongo ya nsembe yake yamachimo,+ ndipo aziphimba machimo+ ake+ ndi a nyumba yake.+

  • Ezekieli 43:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “‘Ansembe achilevi+ omwe ndi ana a Zadoki,+ amene amayandikira kwa ine ndi kunditumikira,+ uwapatse ng’ombe yaing’ono yamphongo kuchokera pagulu la ziweto kuti ikhale nsembe yamachimo.’+ Watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena