Levitiko 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Ndiyeno munthu akachira nthenda yake yakukhayo, pazipita masiku 7 kuti akhale woyera,+ kenako azichapa zovala zake ndi kusamba madzi otunga kumtsinje,+ ndipo iye azikhala woyera.
13 “‘Ndiyeno munthu akachira nthenda yake yakukhayo, pazipita masiku 7 kuti akhale woyera,+ kenako azichapa zovala zake ndi kusamba madzi otunga kumtsinje,+ ndipo iye azikhala woyera.